Ndix models

Ndix models

Share

Born inpoor is not your fault but die in can be your fault

31/03/2025

Kodi ndi bwino k*ti mkazi azidya zimbe?

Ayi, mkazi samayenera kudya zimbe , especially munsewu akuyenda, uku ndikuzitsitsa value koopsa,

Mkazi umayenera uzioneka ovaya , paliponse ukuyenda,mkazi sumayenera yavi yavi chizimbe mmanja,chizimbe kukamwa,

Izizi ndi zakudya zoyenera ma street kid,ghetto yuti Oti asuta suta vyamba osati mtsikana

Umakhala ukuzitsitsa level yako, umakhala ukuzipanga define k*t ndiwe otchipa.

Cuz zimbe ndi chakudya chotchipa koopsa,

Mtsikana zakudya zake ndi pizza,ice cream, burger,hot dog, chips and chicken basi.

Osati pakala pakala kudya chizimbe,

That's why akazi ambiri mukumafunsilidwa ndi amuna a paliponse,cuz amakuonani k*tchipa kwanu ndi dzizimbe zanu mumadyazo.

Munaonako Arya star akudya zimbe? Temis akudya zimbe? Rihanna,Beyonce, bombshell akudya zimbe?

Akazi akumalawi mumadya zimbe chifukwa ndinu achimizi,you're low level

09/03/2025

Namondwe Jude awomba kum'mwera kwa dziko la Malawi kuyambira Lolemba

Nthambi yowona za nyengo yalengeza za kubadwa kwa namondwe otchedwa Jude pa nyanja ya mchere ya India yomwe ikulowera mdziko la Mozambique ndipo ikhudza dziko la Malawi Lolemba likudzari.

Malinga ndi nthambiyi, namondweyu afika madera a Beira komanso Nampula Lamulungu usiku ndipo ayandikira dziko la Malawi Lolemba pomwe agwetse mvula yochuluka ndi mlingo 100 m'maola 24.

Nthambiyi yati ma boma omwe akhudzidwe ndi namondweyu ndi Mulanje, Phalombe, Chiradzulu, Thyolo, Zomba, Blantyre, Balaka, Ntcheu, Machinga, Neno, Mwanza, Nsanje ndi Chikwawa.

Nthambiyi yachenjeza anthu, maka maka okhala mphepete mwa chigwa cha mtsinje wa Shire k*ti namondweyu abweretsa madzi osefukira kamba kak*ti mvula ya mphamvu komanso yochuluka igwa m'madera ochulukawa.

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address

Blantyre