Mandebvu comedy

Mandebvu comedy

Share

This is the official page of MANDEBVU(MAW P*E artist ).

29/05/2026

PONGO WAFA NDIMWANA๐Ÿ‘‡

ANITA ๐Ÿ™:aunt takulandirani,, tinakusowani,, welcome back home aunt

MAI SENI ๐Ÿง‘โ€๐Ÿฆณ:Zikomo tsikana wanga,, kaya munasala bwa?

PONGO ๐Ÿ˜:tinasala bwino opandaso chovuta kaya inu akazanga mwayenda bwa?

MAI SENI ๐Ÿง‘โ€๐Ÿฆณ:ndinayenda bwino, inutu tilonjerana kuchipinda ndakusowani amunanga,, Anita kaya pakhomo pali bwa

PONGO ๐Ÿ˜:aaah mamie mwangofika kumene, tiyeni tikagone zinazo mufunsa mawa,, kmaso anita akuoneke otopa, zintchito zinamupanikiza akagone uyuu

MAI SENI ๐Ÿง‘โ€๐Ÿฆณ: zintchito zapakhomo nde za tsikana kaaa,,, etiii Anita watopa ngat?

ANITA ๐Ÿ™:mwina akudziwa amunanuwo k*t ndatopa, kma ine sindinatope

MAI SENI ๐Ÿง‘โ€๐Ÿฆณ:nde pakhomo pano pali bwa?

ANITA๐Ÿ™:ndisanayankhe ine zapakhomo pano, mwina ayambe uncle kufotokoza zokhuza pakhomo pano

PONGO ๐Ÿ˜:ngat zili zimenezo ndek*t, ndikakuuzani cz ine nde ndatopa ndufuna kugona,, Anita bastu ukagone bwino, mulungu akusamalire usiku umenewu

MAI SENI ๐Ÿง‘โ€๐Ÿฆณ: daddy mwana ak*t sanatope bwanji kd mmakonda k*tchingira akamayankhura,, mmandipasatu mafunso opanda mayankho kma

PONGO ๐Ÿ˜:oky bas pot mwaganiza zambilimbili,, nsiyeni anene bas, ndek*t simumvaso pakamwa panga ntasegula

MAI SENI ๐Ÿง‘โ€๐Ÿฆณ: Anita tandiuze, zinali bwanji pakhomo pano,, k*tengera ndi phone unandiimbira dzana lija

PONGO ๐Ÿ˜:aaah anaimba phone amati chani? Samapeza bwino nthupi? Nde bwanji simunandiuze anaimba bwa?

MAI SENI ๐Ÿง‘โ€๐Ÿฆณ:inutu muli ndi phuma, kd simunachilitsitse?

PONGO ๐Ÿ˜:amakunamizani k*t ndimadwala? Kd mwana uyuu ndiwapakamwa etii

MAI SENI ๐Ÿง‘โ€๐Ÿฆณ:inu musakhale ndi phuma nthawi yanu ifika,, eeeh Anita tafotokoza

ANITA ๐Ÿ™:aunt inetu nkhani yaikulu ndi ija, nnazakuimbirani week yatha, titapita town kukagula zinthu zapakhomo pano,,, amunanu ananditengera ku Bank kukatsegula account, kenako ananditengera ku restaurant kukadya, titamaliza kudya anandiuza k*t tipite ku room tikagone,, en nditakana mavuto anyumba muno anayambira pomwepo

MAI SENI ๐Ÿง‘โ€๐Ÿฆณ:nde zitatero?

PONGO ๐Ÿ˜: ineyo ndimaziwa k*t nyumba muno simmandifunamo, nchifukwa chake munandipanganirana mpaka kumaimbirana phone yachinsisi cholinga muthane nane, zikomo kwambili mmandigwilisa ntchito yokusamalirani pakhomo pano, ine ndaipa lero sopano,, bas ineyo ndikuchoka ambuye akudalitseni pa nkhanza zomwe mwandipanga,

MAI SENI ๐Ÿง‘โ€๐Ÿฆณ:bambo ndinakukondani ndi mtima wanga onse, en ine sindikonda zolongolora,, zonse zimachitika kuno mwanayi amandiuza kma nnalibe nthawi yokuimbirani phone kumakufunsani, iwe anita tamaliza

PONGO ๐Ÿ˜:mwana uyuu ndik*t ndioipa, mukudziwa k*t dzulo anabweresa chibwenzi kmaso okuba nyumba muno,, kma ine ndsyesesa k*teteza chuma chathu, lero mukunditembenukira

MAI SENI ๐Ÿง‘โ€๐Ÿฆณ:musavutike kuziyeresa,, tatenganiso phone yamwana uyu, yomwe munakatenga 30mins yapitayi kwa Muje, plan yanu yonse nnaidziwa kale, monse mmachokera ku chipatala kuzaima panseu kumamuuza muje k*t azabwere kuno mma 10 usiku, munthu anakumvani mukukambirana, en nnamuuza k*t amusatire munthu ameneyo mpaka akaziwe panyumba pake, kenako nnazamutuma muthu emweuja ndi apolisi en anaulura chilichose, ndipo mmene umakampasa lero 150pin nk*t iyeyo atalandira kale 300pin

PONGO ๐Ÿ˜: aaaah amanena muje zimenezo,, muje nde ndani,, anthu inu mukufuna mundipange Chiwembu, oky ndilibe nanu nthawi yolimbana nanu ineyo ndikupita, za phone sindikuziziwa, muje sindikumudziwa, kmaso zonse amanena mfiti ali apayii alibe nazo. Umboni,, umboni wake uli k*t zot ndimafuna kugona nayee?

MAI SENI ๐Ÿง‘โ€๐Ÿฆณ:iwe ine sindinangokhala OC chisawawa ine ndi professional CID, potuma muje k*t azabe phone yauyuu, linali khumbo lofuna kupanga delete video yomwe amajambula ku restaurant ku Limbe,, tsoka ndiloo, video anali ataisamusira mu laptop yake yaku school.

PONGO ๐Ÿ˜:zoipa mwakonza kale, pangani, ineyo mulungu wanga athana nanu, inuyo mukanangonena k*t simumandifuna bas, any way ndapita kma muzandifuna ili ndi dziko,, uyutu sangakukwatireni

MAI SENI ๐Ÿง‘โ€๐Ÿฆณ: banja nnalifuna kma inu ndikuloreni mupite,,, mwina ukuona ngt ndikucheza,, nthawi yomwe ndimaimba phone k*t ndikubwera ija, nnali ntafika kale kuno, kuzasiya apolisi nyumba muno,, en ine nnachitaso k*tuluka ndi galimoto ngat ndikubwera kumene,,,, heyiii ma officers tulukani zamutengeni uyuu, akanenera konko

OFFICER๐Ÿ‘ฎโ€โ™‚๏ธ:bambo pongo tukumangani pa mlandu ovutisa mwana, kuba, kmaso kufuna kugwililira,, chilichose chomwe mungafitokoze chikagwilisidwa ngat umboni pa khothii,,, eeeh tiyeeee galimoto changu...

PONGO ๐Ÿ˜:๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ

NEXT........

(usiku wabwino)Tikaonana pakhothi

29/05/2026

PONGO NDOTOPESA ๐Ÿ‘‡

AMUJE ๐Ÿฅบ:man mission tinaweka za clean,, apaa tisakanganepo fukwa zaka mtonyo

PONGO ๐Ÿ˜:ase tangoperekani phone,zinazo pambuyo

AMUJE ๐Ÿฅบ:inetu nde phone sindingapereke dollar usandipase,,

PONGO ๐Ÿ˜:nde chibwana chimenecho,ukudziwa phindu la phone imeneyo?

AMUJE ๐Ÿฅบ:ngat ili ndi phindu ndek*t dollar upereka,,,paja suumapanganika. Iwee, maka munthu akakuvomereza k*t dollar umupasabe

PONGO ๐Ÿ˜:oky asee, phone yiii, muli dollar zinazake madam anaponyamo kma tsikana uja sakudziwa, nde ndimafuna ndizichosemo, then iweyo utenge gawo lako

AMUJE ๐Ÿฅบ:bas ngat zili choncho mawa uzandipeza kuzatenga phone yiii, tizakachosa limodzi dollar zoo, kma apaa sindingakupase phone,, chomwe umabwelera usiku ngat uno nchani?

PONGO ๐Ÿ˜:ase inetu ndimafuna madam asanafike tikhale tathana nazo, nde ndiitenge ndikangoipanga transfer ndalamayoo mu phone yanga then phone nkaibwezerepo

AMUJE ๐Ÿฅบ: Man mukulingalira moobooka,, ngat zili zimenezo, pangani transfer ndalamayoo phone mwanu,kma phone simutenga

PONGO ๐Ÿ˜:eishh oky chabwino Man tipange chonchi,, ndikupasani half ndek*t inayoo ndikupasani mawa,, kma phone nditenge

AMUJE ๐Ÿฅบ:fukwa chot ndinu anzathu ingotipasani 150 tithane, 50 pin yosalayo muzapereka mukazafuna

PONGO ๐Ÿ˜:ase nsakubisire ndalama zonse zinasala ndine inali 300pin, 50pin. Ndiija nnasiya ku chipatala k*t atituluse ija, 100pin ndi ija nnakupasa k*t adona ako agule chakudya ija, apa k*teroku ndasala ndi 150pin ndendende,,ku account kulibeso dollar ndikudalira madam akafika ndiaponde kenakake, nde inuyo mutenge 100pin k*t ine ndisale ndi 50pin

AMUJE ๐Ÿฅบ: Man mission imeneija siimasala ndi ngongole,, ndipaseni 150 yooo, inu mukatenga mu phone moo, mesa mwati muli dollar umuu. Pangani changu man mwati madam anu akubwera mesa

PONGO ๐Ÿ˜: aaah inu amenewo amuje kundiika khoma etiii?oky muwine ndinuyo,, ndipaseni phone eni dollar yanu iyiii,, moti mukulora k*t ndibwelere padhen opanda dollar nthumba etii?

AMUJE ๐Ÿฅบ: musakwiye nane, anali Ganyu wanga, ndimayenera kulandira ntonyo wanga,, zakwanaso apaaa, eni phone yanu, kma ikazatonyoka mission yanuyii pls ine osazanditchulamo,, akazanu ajaa ndi apolisi sik*ti azandikhaulise ine.

PONGO ๐Ÿ˜:tachokani apaaa, apolisi ndek*t chani? Eishhhh bas tseka kuchikamwako madam akumbaso apaaa๐Ÿ“ฑ.....yes beib...๐Ÿ“ฑ.....wow okay musanalowe kumpanda mundidikire nzasegula ineyoo gatee ndakusowani Akazanga..๐Ÿ“ฑtu.tu.tu.tu..

NEXT .....

29/05/2026

Anthu mmandipezelera fukwa chani?Mawa kwachemaaa. Sungirani Data ๐Ÿคฃ

29/05/2026

Mai awa ndahule๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ
ใ‚šviralใ‚ท

29/05/2026

anati chani. makolo anu, mutawapitisira wachikondi wanu
kwa nthawi yoyamba?
ine anangot mbila yakoyo tisazaioneso pakhomo pano๐Ÿ˜ญ

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address

Blantyre