Chifundo Trojan Mathado
STORIES TO CHANGE THE BAD MIND SET OF PEOPLE FOR GOD'S SAKE!
NEXT :
π
£π
π
π
π
‘π
π
π
π
π
π
π
’π
π
!
12/05/2026
π
π
π
π
π
π
π
¨ π
’π
π
-π
π
-π
π
π
¦ ππ
β
βΆββ β
βοΈ.... " Satana kwake ndi kupha,kuba ndikuonga!...chosa maganizo oipa mkati mwa mwanawanga mudzina la yesu! "
Ndinayankhula mokuwa,mosonyedza kupemphera kuti ndichose bata linali pakati pa ine ndi Linda!
" Chokani apa!
Chiwanda ndinuyo amayi .... ndichifukwa chiyani mukulora satana azikugwiritsani ntchito ? "
Linda anabweza Moto!
Andiyankhula monditsimikidzira kuti ndimachitadi zosayendatu ndi mamuna wake amene ndi mpongozi wanga!
Ndinazimvera chisoni ndipo nsodzi osonyedza kuchimwa kwanga unayamba kutsetserekera m'matsaya mwanga!
" Linda,usalore satana akuchimwitse pokupatsa maganizo olakwikwa....ndine mayi wako and Fundo ndi mwana wanganso ndikachite chinthu chosayenera ngati chimenecho?
Linda,bwelera ku maganizo ako olungama ...mamuna wake amangondiyang'ana kuti ndikhale being and wandipulumutsa !
Usalore maganizo oipa akupangitse kuona zinthu molakwikwa! "
Ndinamuyankhula Linda ndikusuthira naye pafupi,mkumukumbatira mkupitiliza kumuwunikira kuti asadziwe chimachitika komanso akhulupilire bodza lathulo!
Mapeto ake,Linda anapezeka akulira motsitsima m'manja mwanga,kwinaku akuyankhula mondipepesa kuti ndimukhululukire chifukwa anaganiza molakwikwa!
" Mwana ndi mwana...sangavute make! "
Ndinaziyankhulira mobwekera mkati mwanga nditadziwa ndamugonjetsa,wakhulupilira pakati pa ine ndi Fundo palibe chinachitikacho kupatula kundithandiza ndikhale bwino.....
Eya ndikhale bwino akandigwiragwira mkundifiklisa kumene amuna anga sanandifikiseko!
" Mamie....ndikukhulupilira simunamwe pain killer uja ndichifukwa mumalira ndi ululu wa mutu umakuvutaniwu!
Kuteroku,nanenso ndimabwera kuzakuoangani check,ndimazakupasaninso mankwala kuti mumwenso! "
Modekha,akundiyang'ana mondimvera chisoni komanso mopepesa, anandiyankhula Linda!
" Osadandaula mwana wanga,ndimadziwa umandikonda, ndichifukwa nanenso ndimakukonda!
Apongozi andithandiza ndili bwino panopa....pita ukagone mwana ndi mamuna wake akukudikira! "
Ndinamuyankha Linda, andiyang'ana mondimvetsetsa,anatembenuka mkuyamba kuyenda ulendo wa ku chipinda chawo,koma anatembenukanso mkundiyang'ana,kuyang'ana kusonyeza kusandikhulupilira!
Kenako anapitiliza ulendo wakewo!
KUCHIPINDA KWA LINDA
" Ndichifukwa chiyani towel yako inali itatundumuka pa lisani ukutuluka kuchipinda kwa amayi anga kuja? "
Linda,ndi mkwiyo anamufunsa Fundo!
Fundo sanayankhule ngakhale anamva funsolo,anangoyankhula zosamveka mkutembenukira mbali inayo mkunamizira kupitiliza kugona!
KUCHIPINDA KWA AMAYI A LINDA
Usiku umenewo sinagone,ndimangolinhalira zinachitikazo kuti ine ndi Fundo tapulumuka lokumbakumba chifukwa cha condom!
Linda akanatipezelera,ngakhale akanakhala kuti anali asanalowe,ananandimva ndikumulilira mamuna wakeyo Ali pamwamba panga!
Kutacha,ndinayankhula a ndi Linda kuti ndikuyenera ndizipita!
Ndimafuna ndipewe zambiri ngakhale ku town kusandiyankhula and ndimasanzika ndi mtima umodzi chifukwa ndinali ndisanathane ndi Fundo bwinobwino!
" Mamie,mwazi was mawa ndikukayamba ntchito,nde ndimafuna mukhalekonso mwezi wina,ndikufunafuna wantchito Inu muzindisamalirako mwanayu! "
Linda anandipempha,ndipo anandilonjeza awayankhula bambo ake kumudzi ndikhalenso mwezi wina and zinatheka!
Mwezi umenewo,ngakhale ndinali nditapanga chiganizo Fundo akayesetsera kundigwira ndimuyankhule mau a chakwanu leka,koma ndipamene timaoitilizabe nyansi zathuzo!
Tinafika pa uchitsiru,Linda anangoti akasutha pang'ono,tadyana,onse akapita ku ntchito,Fundo amathawira mkubwera kunyumba kuti tizadyane....oooh Pena,ndimakhala ngati mayi a Linda,nthawi zina mkumakhala ngati mkazi wachiwiri wa Fundo!
Chimene chimandichitikira sindimachimvetsa!
Tikamaliza kupanga zathuzo,ndimamva kunyansidwa komanso kuzimvera chisoni!
Koma Fundo amati akabwera mkuyamba kundigwiragwira,ndimalephera kumuretsa mpaka amapezeka ali pamwamba panga kapena ine pake tonse buno bwamuswe Mai ndi mpongozi wake!
Week yomaliza ya mwezi wa chiwiri ndili pakhomo pa awiriwo,madzulo wina,ine ndi Linda tikuphika ku kitchen,ndinayamba kuyankhula,kumukumbusa za ulendo wanga obwelera kumudzi....
Koma,ndisanatulutse mau,m'mimba mwanga munatembenuka,ndinatenthedwa ndipo chinseru chosakhala being chinandigwira!
Sindikanachitira mwina,koma kuthamangira pa sink mkukasanza!
Ndinasanza,kwa kanthawi,koma zosanza zochepa ndipo nseru sunachoke nsanga!
" Mamie .....chavuta ndi chiyani Kodi mutu uja wayambiranso! "
Linda atandiona anandithamangira,mkundigwira pa nsana ndi mumtima mkumandipanga zoti ndisoiye kusanzako!
" Ayiso honey....simutu and sindikudziwa ndi chiyani?
Mwina chifukwa dzulo lija ndinadya mochedwa! "
Ndinamuyankha Linda,koma ndimakaikira kuti itha kukhala mimba chifukwa sindinaphwanye madzira mwezi umenewo!
" Akhoza kukhala Malungo amenewa!
Ndimuitane Fundo akuperekezeni ku chipatala...."
Anatero Linda akundiyang'ana mondimvera chisoni!
" Fundo? "
Ndinaziyankhulira mozifunsa!
π FUNSO.....Kodi mayi a Linda,pachiyambi ataona mpongozi wawo wawagwira matako komanso mchiuno amayenera kuchita chiyani kuti zinthu zisafike apa?
Yankhani momveka bwino kuti wina wake,kwinakwake yankho lanulo lizamuthandize asazapezeke akulakwisa ngati Mai a Linda !
Nkhaniyi yatsala ndi Part imodzi, ngati simunandionese izakuphonyani chifukwa sindimaponyanso share ku ma groups!
π
£π
π
π
π
π
π
π
£π
π
π
€π
π
!
Β©2026 Chifundo Trojan Mathado The best writer and story teller of all the time!
11/05/2026
ADONA, AKAZI AWO A BWANA ANGA ANASINTHA KHALIDWE MOSADZIWIKA BWINO, ANAYAMBA KUVALA ZAZIFUPI,ZOWONEKERA MKATI NDICHOLINGA ANDIKOPE!
KOMA NDIMATI NDIKAGANIZIRA NKHANI YA JOSEPH NDI MKAZI WA POTIPHAR YA BIBLE NDIMAWAPEWA...KOMA MAPETO AKE....π
π
£π
π
π
π
‘π
π
π
π
π
π
π
’π
π
π
Ώπ
°ππ π
Έπ
Έπ
Έ
βοΈ....nditafika pakhomopo, anthuwo anandilandira bwino,ndimakhala nawo limodzi,anandipasa room ina ku ma quarters,imene ndinagona koma chichonse ndimachita mnyumba yawoyo!
Mabwana angawo,amandikonda ngati mwana wawo yemwe, chifukwa cha ichi,ndimawaitana kuti dad and mum!
Nawinso ana aja,amandilemekeza osatengera kuti ndine wantchito,akandifuna amanditana Uncle Fundo!
Ntchito imayenda bwino ndithu,ataona makhalidwe anga,abwana amuna,anayamba kundidalira komanso kundikhulupilira,kotero zinthu zambiri za business yawo yopanga supply food stuffs ku ma schools ndimayendetsa ndineyo!
And mu zonse,ndimayendetsa mopanda chinyengo chifukwa ndimadziwa pakumwa saonongera ulova unandikanda kwambiri nde sindimafuna kupanga mistake ndibwelerenso kumudzi!
Moyo wanga unasintha,kaonekedwe,kavalidwe komanso,ndimatha kukhala ndikupeza zinthu zimene mbuyomo ndimangosilira!
Chifukwa chakuti sindimagula chakudya komanso kulipira rent, malipiro anga,ndimatumiza kumudzi kuti anthu andiombere njera,chaka chinacho ndimange nyumba chifukwa sindimafuna kukafikiranso mnyumba mwa makolo anga ntchito itakhala kuti yatha mkubwelera kumudzi...paja mwambi umati ntchito ndi mwamba!
Kumbali ya mwabwana angawo,amakondana kwambiri,muchina chilichonse, amachitira limodzi,ngakhale kudya,palibe amadya payekha,wina akafika nsanga pakhomo,olo akhale Ali ndi njala,amadikira mzake afike!
Kumbali ya ma phone,aliyense amagwuritsa ntchito phone ya mzake ngati yake yomwe,akakhala limodzi,palibe amene amakhala pa phone mkumakomedwa ndi social media ngati achitira mabanja ena...iwo amalemekezana komanso kupasana attention nthawi zonse!
Izi,zimandipasa chidwi,komanso ndimawasilira kwambiri!
Koma,zinthu zinayamba kusintha kuyambira usiku wina!
Tonse,tinadyera limodzi,tinacheza,bwana anga amuna anandiuza zoyenera kuchita ndikachokera kosiya ana mma schools amaphunzira,kenako ndinasadzika,kufunirana usiku wabwino ine mkupita ku quarters mkukagona!
10:49 pm,ndinamva phokoso mnyumba yayikulu ija,phokosolo limakulirakulira,apa,ndinadziwa ma bwana angawo akukangana!
Izi,zinandidabwitsa kwambiri chifukwa sindimaziyembekezera kwa anthu amenewa potengera m'mene amakonderana!
Ndimangonena mu room yangayo,pena osamathamangira kulowelera za anthu ena,makamaka monga mabwana!
Zina zimakhala nkhani zawo za chinsinsi and moreover,amakangana ku chipinda mwina wina mkukhala kuti ali maliseche,nde sizinthu zabwino!
Mkanganowo unakula,zimamveka atuluka ku chipinda,afika pa sitting room,posakhalitsa,ndinamva kulira kea makofi,adona anayamba kulira!
" Atha kuphana anthuwa! "
Ndinaziyankhulira kwinaku ndikuvala bwino kuti mkalandise awiriwo!
Ndikutuluka,ana awo analinso akubwera ku room yanga ija,kuzandiuza za makolo awo aja....
" Uncle...fulumirani dad akuwamenya Mamie mukawalandise! "
Mwana wamamuna uja anandiyankhula mondipempha,pamene wamkaziyo amangolira!
Zinthu zosakhala bwino,ana amasangalala akamaona makolo mukukondana osati kukangana kumenyana!
" Ungafike mpaka pondinena kuti mwana wangayu siwanga kma amuna amzanu anangokuikiramonu? "
Awa anali abwana angawo kufunsa mokalipa,mokwiya komanso monyansidwa ndi mau anayankhula adona aja....
Ndinawagwira dzanja abwanawo, chifukwa anali atakunga mbama ina kuti igwere pa tsaya la akazi awo aja!
" Ngati a ex akowo unawapasa mimba ndiweo bwanji ukukanika ine? "
Anayankha adonawo mopanda mantha ataona owalandisa watulukira!
Ndinawakumbatira abwana aja,kuiwala ndi boss wanga mkuwakokera kutali ndi akazi awo aja!
" M'mesa ndi chifukwa cha zi ma contraceptive zakozo,zimene zikumandipangisa ine kukhala ngati opanda mbeu ...."
Anayankhulanso abwanawo,ukali uli paliponse!
And aka,kanali koyamba kuwaona abwana angawo atakwiya chifukwa nthawi zonse amakhala omwetulira!
Koma nyengo ndi nthawi,munthu umazafika pokwiya ngati siwenso!
Nditawalandisa,amunawo,anangotenga ma key a galimoto mkutuluka,and tonse ine ndi adona sitimadziwa akupita kuti....
Ndinawafunsa adonawo chatsitsa dzaye kuti nditolere nkhani yavuta mpaka awiriwo afike pokangana mwamtundu umenewo?
Komabe,ndimadziwa kuti nkhani yake,ikuyenera kukhudza mwana nde onse akuyang'ana blame kuti wina Ali ndi vuto!
Adonawo mtima utakhazikika anayamba kundifotokozera mitere......
π TIKHALE LIMODZI MU PART 4
Ndipangeni kuti ndikaponya nkhaniyi isamakuphonyeni!
Β©2026 Chifundo Trojan Mathado The best writer and story teller of all the time!
γviralγ·fypγ·γviralγ·
Good morning fans!
Wishing you a blessed Monday!
π
£π
π
π
π
‘π
π
π
π
π
π
π
’π
π
Is Loading βοΈ
Time out!
Ndikulemba me and ME AND MY SON-IN-LAW
Click here to claim your Sponsored Listing.