Frend
Reminding the ummah all praise is due to Allah who teaches a person things he doesn't know..
01/06/2026
Osamuka! Osamuka! aiwala ujeni padenga🤣🤣
06/05/2026
Akumati ndi ma graduate.
Alinawotu ma degree.
Amati ndi ophunzira iwowo.
Chipanda chodzadza ndi utoto wa maphunziro adamwera iwowo.
Amati ndi ozindikiratu iwowo.
Anawerengatu ma book ochuluka.
Amadziwa zinthu zosiyanasiyana.
Koma zoti chisilamu n'chipembedzo monga chilichonse.
Si chilankhuro komaso mtundu wa munthu.
Koma n'chipembedzo cha aliyense.
Sadziwatu iwowo.
Aliyense ooneka mwa chiluya.
Ooneka mwa chimwenye ndinso mwa chiyao.
Okhala nalo dzina lomveka mwa chiluya.
Olankhura chiluya ndinso chiyao.
Ameneyotu ndi msilamu kwa iwowo.
Zoti Arabic ndinso chiyao.
Ndichilankhuro monga chingerezi, chipwitikizi ndinso chichewa.
Sadziwatu iwowo.
Komatu iwowo, amati ndi ophunzira.
Amati ndi ozindikiratu iwowo..... .............to be continued
Rafiq Saidi Assami
MAV TALK SHOW
Indee Voices
HûssêÃñ MâÃlôs
Brown Chrispine
Ineyo nduona ngati mnyamatayu za ma nasheed zija zinkamuchedwetsa, inu muona bwa? 🤣
Omar Ussi zabho?
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the public figure
Address
Lilongwe