Tipakule
Find love here, banja , chibwez or hit and run. Timagawa ma cross pano
Apakuli tipaseni mamuna usiku pano tikagone kwao
Km akhale WA phanvu chifukwa ine chibaba chandipola kwambili.
Am in lilongwe.
APAKULI ndikufuna nkaz odziwa kuphika bwino lelo Abwele pa home pompano km no s*x, tinvane nae around mzuzu
24/05/2026
Hello big man! Muli bwanji?
Ndine mnyamata wa zaka 27 ku BT chilimba. Ndikufuna undilumikizise ndi mkadzi wa around yemwe akufuna Serious relationship yothera banja. Akhale wa zaka malire 23. Akhale okutha kucheza kwambiri chifukwa ineo ndimagwira ntchito koma nthawi zambiri ndimakhala free.
Please akhale oti alibe chibwezi komaso wa serious. Ineo ndimagwira ntchito m'boma koma iyeyo akhoza kukhala aliyense or osagwira ntchito. Akhale okonda communication.
Akapezeka mundilankhula ku inbox.
Apakuli ndili Lilongwe town ndipaseni mamuna hit and run tinvane
Click here to claim your Sponsored Listing.