Mayani Musik

Mayani Musik

Share

AFRO_REGGAE DANCEHALL ARTIST /RECORDING PRODUCER & MASTERING ENGINEER FROM BLANTYRE MALAWI FOMERY KNOWN AS FYAH BWOY

30/11/2025

Kudzikumbitsa masiku amake dzana๐Ÿ˜๐Ÿ˜‚. playing with my big brother's songBusy Signal ๐Ÿ˜œ

23/11/2025

Muli ndi nthawi? tanvelankoni ka nkhani aka๐Ÿ˜ full story ili ku TikTok.

and don't forget to check out our new song "Umuiwale" you can stream on YouTube or purchase via pay changu if you want to download. all links in the comments let's gooo๐Ÿ”ฅโœŠ๐Ÿ”ฅ

21/11/2025

Good morning family. Pali kusintha nyimbo yanu ija ituluka 12:30 PM.

kwa amene uthenga sunakupezeni
tibweleze kuti mukhala ndikuthekela kokhalanayo nyimboyi ndi ndalama zokwana K1000 yokha basi. Ndipo kagulidwe kake ndikamakono kosavuta tiponya link ndi kufotokozaso momwe mungachitile kuti zitheke.

Thank you for always supporting us. !
!

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Ntchisi?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address

Ntchisi