Mym ray
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mym ray, Digital creator, Raphael y mulema, Salima.
08/01/2026
aTrump timangochezatu musazitengere serious chonde
09/12/2025
SOFUTATU SITHU SAKE
COME & READ with me
ABWINO SAKHALITSA!
Sizinkatheka kupereka chitsazo chamunthu wamzeru, ofatsa, waulemu, ozichepetsa kapena opatsa osatchula dzina lake. Kunena zoona ngakhale nane ankandipatsa chidwi.
Munthawiyi ndinali ndiri kusukulu yanga yapulayimale, Alifoso anali mzanga yekhayo wapamtima, Alifoso anali wakhalidwe labwino komaso odziwa kucheza bwino ndiathu. Timat tikaweruka kusukulu, iye amatanganidwa ndikuwerenga zomwe taphuzira patsikulo. Ine ndiazanga tinkakhalira kumunena poti ankatikalipiritsa kwamakolo anthu.
Chifukwa cha kulimbikira kwake, Alifoso amakhala nambala yabwino zotsatira zamayeso zikatuluka. Titalemba mayeso athu astandade 8, Alifoso adasankhilidwa sukulu yogonera konko yam'boma mwathu pomwe ine adandisankhira sukulu yoyendera yammudzi mwathu.
Koma kaamba kamavuto azachuma Alifoso sadakwanitse kupita kusukulu yomwe adasankhilidwa, ...
NEXT part is coming soon!
KUSELI KWADZIKOLI
01/11/2025
Ndakadzidzi avutawa
Nde pali anyamata ena , pic yakazi awo kungodutsa koma yankaz wanzawo uva "so pretty" chimakhala chiri chan koma 😳😳😳
Kod mumatan kuti mukhale ndma followers ambiri?
Moyowu uli ngati hlhhfxfvbjtedg
, ndiosavetsetseka. GOOD morning
There was an important job to be done by ANYBODY
EVERYBODY think that SOMEBODY will do it
NOBODY did it thinking that SOMEBODY will do't
who can do it if you can not do it?
it is our renspossiblity!
by Mym ray ]
RENSPOSSIBLITY
Mateyu 7:13-14 Lowani pa cipata copapatiza; cifukwa cipata ciri cacikuru, ndi njira yakumuka nayo kukuonongeka iri yotakata; ndipo ali ambiri amene alowa pa ico. Pakuti cipata ciri copapatiza, ndi icepetsa njirayo yakumuka nayo kumoyo, ndimo akucipeza cimeneco ali owerengeka.
18/10/2025
Ndichani chimene simuzamuyiwala nacho nkulu uyu?
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Salima