PortHerald Press

PortHerald Press

Share

Licensed Online Media House.We are in Old Priest's House,Ngabu-Chikwawa MW

The best online publication that provides catchy and tangible breaking news.

20/06/2026

Mtsogoleri wa Football Association of Malawi, Fleetwood Haiya, watsimikiza kuti adzapikisana nawonso pa mpando wa Pulezidenti wa FAM pa zisankho za chaka chamawa.

Kale Haiya adanena kuti sadzakhala pa mpando kwa zaka 19. Koma tsopano wati pali ntchito zina zofunika zomwe sanazimalize, ndipo akufuna kubwerera kuti akazimalize.

"Ndili ndi masomphenya ena omwe ndiyenera kuwamaliza. Sizingatheke m'kanthawi kochepa chonchi," adatero Haiya.

Ntchito zake za zaka zapitazi zikukusangalatsani kapena ndi nthawi yosintha magazi?

(BLANTYRE)

Telephone

Website