Lai
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Lai, Digital creator, Zomba.
25/02/2026
"DZUKANI KWACHA☀️🫵"
MLANDU WA MWANA WA MALEMU WA PRESIDENT WAMKALE WA DZIK0 LA ZIMBABWE R0BERT MUGABE'S S0N YEMWE ANAMBERA GARDEN B0Y WAKE KU JUBECK
Mt0lankhani H0pewell Chin0,n0 anakapanga chipikisheni ( research) ndip0 adapeza kuti Chatunga Mugabe Hyde Park H0use , nyumba yake y0mwe akukhara Mwana wa Mugabe inagulidwa mu Chaka cha 2017.
Pamene bamb0 ake akaladali ndi Mphanvu ( when his father was still in p0wer) , Ndip0 Antigura kwa Ndalama z0kwana R43, Million pafupi-fupi US$3.2 Million Dollars, pa nthawi y0.
Ndip0 Chatunga ata0nekera ku C0urt , ndip0 anavala kasukumba k0dula manja ( a Moncular Maya puffer) y0mwe mteng0 wake US$2,556 pafupi-fupi Ndalama z0pitilira ( R40,000 Rand) ch0nvala chim0dzi .
Ndalama ya ch0nvala chim0dzi chimenechi ili ngati Malipir0 0nse amunthu 0gwira ntchit0 b0ma ( same like civil servants saraly yearly) chaka ch0nse dzik0 la Zimbabwe.
Ndiye apa mwaw0na n0kha andalewa z0mwe amapanga sindikutchula dzala munthu wa ndale aliyense wa ku Malawi, k0ma ndati andale.
Click here to claim your Sponsored Listing.