Leadership and Development
In periods where there is no leadership, society stands still.
05/06/2026
Yesterday, our team supported Early Childhood Development ( ) activities at Mpinganjira Community-Based Child Care Centre ( ) in Mangochi.
Happy World Environment Day
03/06/2026
Our team is attending the Umunthu Social Impact Forum in Lilongwe, joining various partners and stakeholders in an effort to create positive social impact in Malawi.
30/05/2026
Nduna yowona zakusasiyana pakati pa amai ndi abambo, ana, ulumali ndi chisamaliro cha anthu, a Mary Navicha, yadandawula ndikukula kwa chiwerengero cha ana omwe akumapezeka akupemphetsa m’misewu ya m’mizinda ya m’dziko muno.
A Navicha ati nzomvetsa chisoni kuti pafupifupi theka la anawa ali ndimakolo awo komanso makolowa ndiwo amawatuma kuti azikapempha.
Ndunayi yanena izi lero pa mwambo okumbukira tsiku loganizira mabanja padziko lonse komanso ana omwe amapezeka ndikukhala m’misewu, omwe wachitikira pa bwalo la zamasewero la sukulu ya pulayimale ya Lunzu m’boma la Blantyre.
Ndunayi yadzudzulanso mchitedwe omwe wakula m’dziko muno opangira nkhaza ana monga kuwagwililira, komanso kuwapatsa zilango zowawitsa akalakwisa.
M’mawu awo, mfumu yayikulu Kapeni ya m’boma la Blantyre, yadzudzula mchitidwe wa abambo ena omwe akumangobereka ana ochuluka koma osamawapatsa chisamaliro.
Mfumu yandodoyi yati mchitidwewu ukupangisa kuti ana ambiri m’dziko muno azikhala moyo ozunzika kuphatikizapo kupezeka akugona, kuyendayenda komanso kupempha mmisewu ya m’mizinda ya dziko lino.
Bungwe la YONECO mogwirizana ndi boma komanso mabungwe ena monga Project Hope Namibia, SOS Children’s Village, YODEP, ndi ena ndiwo anakonza mwambowu omwe wachitikira pamutu oti: Mabanja olimba komanso osasankhana ndi maziko amoyo wabwino wa ana.
25/05/2026
YONECO joined various institutions at the 36th Malawi International Trade Fair (MITF) in Blantyre for Career Day activities aimed at empowering students with career guidance and future opportunities.
The event brought together learners from various schools across the city, providing them with an opportunity to interact with professionals, explore different career paths, and gain valuable knowledge to help shape their futures.
Through the sessions and discussions, students were encouraged to make informed educational and career choices while building confidence to pursue their ambitions.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the organization
Telephone
Website
Address
Zomba