Zomba Diocese
Evangelization for salvation of humankind
Kwakoma ndi ku St. Charles Lwanga parish ku fund-raising ya Laity Council after the Big Walk. Please support us!!
09/05/2026
Ulendo wa ndawala womwe cholinga chake ndikufuna kupeza ndalama zothandidzira bungwe la Akhristu eni ake (Laity Council) wayamba tsopano.
Ulendo-wu wayambira pa Naisi ndipo ukathera ku St. Charles Lwanga parish ku Zomba.
Ndalama zomwe zipezeke pa ulendo-wu ndi zoti zithandize bungwe la Laity Council ku Zomba Dayosizi kukhala lodzidalira palokha kudzera mu ntchito ya ulimi.
Ambuye Alfred Mateyu Chaima, Bishop wa Dayosizi ya Zomba, ali nawo pa ulendo-wu.
NANUNSO M***A KUTHANDIZAPO PA BIG WALK IMENEYI. NGATI MUKUFUNA KUDZIWA ZAMBIRI, IMBANI PA: 0999728026 KUTI MUPEREKE THANDIZO LANU LERO KAPENA KULONJEZA/PLEDGE.
M***ANSO KUPEREKA THANDIZO LANU KUDZERA KU NATIONAL BANK ACCOUNT NUMBER IYI: 1010273605 KAPENANSO PA AIRTEL MONEY KU NUMBER IYI: 0999728026.
ZIKOMO CHIFUKWA CHA THANDIZO LANU. MULUNGU AKUDALITSENI!
05/05/2026
Join us and support us!
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the place of worship
Telephone
Website
Address
Zomba
00265