GoalLine Media
super league football live
01/02/2026
Ngati njira imodzi yofuna kulimbitsa malo ena mutimu ya FCB Nyasa Big Bullets, akulu-akulu a Mapale, alembera kalata Silver Strikers kufuna ntchito za mphangala zawo George Chikooka, MacDonald Lameck, Uchizi Vunga komanso Festus Duwe.
Pep Guardiola manager wa team ya Manchester city mkulu uyu azagwa ndi BP taona kuzigwetsa pansi amaona ngati mpira ukupita kukalowa
Team ya FCB Nyasa Big Bullets yatsutsa kuti Mphuzitsi anamupeza kale angofuna kuphimba maso anthu potumiza ma kalata awo ofuna kulembera ntchito ngat mphuzitsi wa teamyi