Bullets Forever
π’Tsatsani malonda anu ndi Bullets Forever β½π¬
Once Maule always Maule β₯οΈπ€
Ndani amene angalosere position yomwe Bullets ithere mu First Round ya FDH Premium League? Wamwayi m'modzi will earn K5,000π°
Ndi timu iti yomwe ikagonjetsa FCB Nyasa Big Bullets mumanva kuwawa kwambiri kuposa tikagonja ndi matimu ena?
26/06/2026
Maule tikhale tikubwerera pa Home ground yathu pa Kamuzu Stadium shortly following it's qualifications. Tikangobwerera pabwalo apapa League yaikulu ya ikhala kuti yapita ku Bullets basi.
System of play ya Wedson Nyirenda ikufunika ma stadium ngati awawa ndipo matimu kudzakhala kuwusaka mpira osati sewero ππ€£.
β€οΈπ€πͺ
Follow π Bullets Onlineβ
Masters Security ikufunika kuyipuntha ndi zigoli zingati Monday lino?
Tchulani legend m'modzi wa FCB Nyasa Big Bullets amene ankakusangalatsani pa chikopa π
Ngakhale mwatisinthila bwalo koma Bullets idzapambanabe munjira iliyonse π
22/06/2026
Next Game ulipo wa nkhodzo za pusi pa Mpira Stadium ποΈ munzinda wa Blantyre. FCB Nyasa Big Bullets ya π Masters Security ya π₯.
Sorry Mponda watola Joker ππ€£π€£π₯π₯.
β€οΈπ€πͺ
Kodi Maule m'mene zateremu tabwera pa number chani pa log table?
21/06/2026
Yamikani Mologeni wamfupi ngati Zakeyu koma waluso ngati Chiomba Nkhanga π¦
.
Mologeni nkatundu mwanayu π₯π₯π₯π₯.
β€οΈπ€πͺ
Koma kunena zoona Wedson Nyirenda wabweretsa mpira okongola ku Bullets timpatse ulemu wapadera π₯π
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Port Elizabeth
6000