CapeStars

CapeStars

Share

CapeStars is a liquor brand inspired by Cape Maclear, most beautiful amazing historial tourist site.

23/05/2026

"Onsewo mukuwaona ukowo, akumwa Capestars"

Ngati muli ku Cape Maclear, khotani pa Sangalala. Capestars mumpeza ndithu.

Weekend yanu ikuenda bwanji?


🥃

20/05/2026

Sun out. Views out. Capemac in hand.
Tsiku lanu likuenda bwanji?


🥃

13/05/2026

Kunja nkwa dzuwa uku. Mwinatu nkutheka muli ku Mangochi, kapena muli ndimaganizo olowelera chakumeneko, ndipo nkhawa yanu ili pokuti mumpeza pati Capestars?

ndi malo omwe ayandikana ndi Ekhaya. Pamenepatu mukapeza Capestars wankuntima kwanu, pamtengo wabwino.


🥃

11/05/2026

Every sip tells a lakeside story. 🌊
Smooth enough for the lake breeze.


🥃

05/05/2026

Akuti akaka ndika fruit after meal.😂
Anena anena basi, ife ndi ndani kuti tikane?

Masana abwino konse komwe muli.


🥃

Want your business to be the top-listed Grocery Store in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Telephone

Address


2 Bank Road, Sunnyside
Blantyre

Opening Hours

Monday 09:00 - 17:00
Tuesday 09:00 - 17:00
Wednesday 09:00 - 17:00
Thursday 09:00 - 17:00
Friday 09:00 - 17:00
Saturday 09:00 - 17:00