Islamic Issues II
Iyi ndi Page yomwe m***a kutumiza nkhani zokhuza chipembezo cha Chisilamu, , ndinu olandilidwa
KODI FODYA MU CHISILAMU NDI HARAM KAPENA MAKRUH?
Brothers and sisters , tidziwe Kuti sibwino kumalankhula zinthu zopanda umboni mu din yathu.
Pali kusiyana kowonekera pakati pa ma MAKRUH NDI HARAM
Haram NDI chinthu chimene Allah waletsa osati kuloleza.
Pali zimene Allah analoleza osati kulamulila
Monga mitala.
Mulungu waletsa chiwerewere, kuledzera, katapila, kudya nkhumba, zakufa zokha, magazi , zozingidwa ndi anthu omwe SA asilamu.
Kuletsedwa uku mwachindunji , kupanga izi NDI Haram.
Tsono MAKRUH ndizinthu zimene zili zosakhala BWINO mnsilamu kupanga , kima ukapanga sizikuteñgera ku uchimo.
MAKRUH ndimachitidwe omwe ukawakakamila atha kukuwonongera tchito zabwino.
Zitsanzo NDI
Kusunga zikhadabo ,
Kusunga zikhadabo si Haram koma MAKRUH
Zikhadabo zikhoza kusunga najsi mkuwonobga swala yako.
Tikafika kunkhani ya FODYA Ili mmagawo awa
1. FODYA amaika umoyo wa munthu pa risk
2. FODYA wina amasokoneza kaganizidwe.
3. FODYA ndichinthu chomwe mnchovuta kuchisiya.
👉 Chilichonse choika umoyo wamunthu pachiwopsezo ndi Haram, Allah akuti 👉 usaziphe wekha
👉 Chonse chosokonesa bongo ( kullu muskirin ) mncholetsedwa chili mu gulu la zoledzeretsa.
Automatically FODYA NDI Haram osati MAKRUH..
Follow this page for more updates
Click here to claim your Sponsored Listing.
Telephone
Website
Address
Blantyre