All connection connecter Agent

All connection connecter Agent

Share

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from All connection connecter Agent, Business Center, Blantyre.

29/10/2025

page for sell contact us on this number 0993500406 call or sms

It's 62k followers hit us

23/09/2025

Mukafuna ma remedy amakhwala alionse tipezeni pa call or sms 0993500406 tikuthandizeni

23/09/2025

*mankhwara awa omwe ambili mwakhara munivutisa kuti mukuwafuna*🍃🍃🍃🍃🍃🍃🍃🍃🍃🍃🍃

🍃masikuwa kwachuluka vuto lokhuza kufooka kwa chida Cha abambo kuchipinda makamaka kusazuka kwa chida mosakwanira ndithu inde vutolo si la inuyo nokha ayi koma tilipo ichuluka zedi bolani ngat iweyo chikumazuka nikumenyako imozi mofoka momo pomwe azako ena sichizuka komwe ayi ndithu

🍃Inde vutolo zikhoza kutheka kuti wina wake anakupanga chipongwe Cha mwamuna aligone kuti chidacho chisazagwileso ntchito mokwanira ayi nipo zikuvutadi kugwira ntchito mokwanira

🍃komano mankhwara okozedwa Kare awa alipo ndithu tipeseni ngati MKUFUNA mutap nga nokha komwe Inu mli

*Pezani izi*

🍃phungura
🍃mpungulila
🍃mkwapukwapu
🍃 gondolosi
🍃 chamwamba

🍃zosezo mutenge mizuyakeyo nikuyisinja bwino nikuika mubotolo
la 2liters nikuikamo mazi nikukhuchumula kwambili

🍃mupaka ziyambe kutulusa nthovu chifukwa nthovulo nde mphavu za mankhwara awo etu
Ndiye muzimwa kawili pa siku mamawa ni mazulo kwa 4days muzakhrara mboni yanga ndinthu kuti mwabereka mwana kwina kwake

Natural medical treatment

Sms 0993500406

23/09/2025

*_KUTETEZA BUSNESS KWA OKAWA_*

kutheka ndi inu mmozi mwa amene mumagulisa kwambiri malonda anu koma munthawi yowelengela ndalama ndi mmene mwagulisila nzotsiana,

ai musadandawule thandizo mwalipeza pano👇

THANDIZO

choyamba pezani masamba a (kankhande) masamba (amsuka chuma) kanyama kotchedwa kamfadala. Kàmbewa kaja timati swiswili

Zonsezo muzisinje mkusoka kachithumwa mukasiye malo omwe mumasiya ndalama yanu

Pamenepotu mumakhala kuti mwateteza ndalama yanu

pezani mizu yansolo ndi mizu ya nsuka chuma ija mkusakaniza ndi nsalu ya kumwezi 👇

mutemele mmbali mwa mutu ndi manja anu izi zimakuthandizilani
Kuiziwa ndalama ya chinyengo

Ofuna zokoza kale inbox bas kuvana kulipo

Pangan follow page ino kt ma post asamakuphonyeni osaiwala kupanga like post kumeneko nde kundithokoza kwake kt ndibwereso ndi post ina ondifuna pa watsaapp

0993500406

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address


Blantyre