Mechro

Mechro

Share

Mechro Limited - Innovating Agriculture! Embark on a journey where tradition meets innovation, and technology harmonizes with the land.

28/05/2026

Nkhokwe, thumba la a Malawi. 🌽

Kodi mukudziwa kuti mpaka 30% ya chimanga, nyemba, nandolo, kapena khobwe wanu chimaonongeka chaka chilichonse? Osati kumunda, koma ku nkhokwe kapena mmatumba anu ngakhale muthire mankhwala ophera tizilombo tanankafumbwe?

Mechro Limited yapanga Nkhokwe Harvest Storage Bags kuti tithandize alimi kuno ku Malawi kusunga zokolola zawo bwino.

βœ… Thumba la Nkhokwe la makilogiramu 50
βœ… Limaletsa mpweya kulowa mthumba lanu. Kupha tizilombo tonse popanda mankhwala
βœ… Sililola chinyontho kuti chilowe mthumba lanu. Chimanga chimatetezeka.
βœ… Malangizo pa thumbali analembedwa mu Chichewa. Chifukwa timasamalira alimi a m'dziko la Malawi ndi maiko otiyandikira kuti agwiritse ntchito bwino.

Zokolola zimakhala zotetezedwa, kuthetsa kuonongeka kwa chakudya kuchoka pa 30% kupita pa 5% yokha!

Alimi oposa 6,500 ku Malawi akugwiritsa ntchito Nkhokwe Bags kale.

Mukufuna kusunga zokolola zanu bwino chaka chino? Tilankhuleni:

πŸ“ž +265 881 606 174
πŸ“§ [email protected]
🌐 mechro.io
πŸ“Chichiri Trade Fair Grounds, Stand Number 5G, Blantyre

Matumbawa akupezekanso kwa ma agro-dealer otchuka mu mdela lanu.

Want your business to be the top-listed Computer & Electronics Service in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Telephone

Address


Malawi Confederation Of Chambers Of Commerce And Industry (MCCCI), Chichiri Tradefair, Stand Number 5G
Blantyre

Opening Hours

Monday 08:00 - 16:30
Tuesday 08:00 - 16:30
Wednesday 08:00 - 16:30
Thursday 08:00 - 16:30
Friday 08:00 - 16:30
Saturday 08:00 - 11:30