Altitude Technologies

Altitude Technologies

Share

Leader of Pre-owned and New Electronic Devices in Malawi ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ

30/12/2023

Kwasala ma ola 24 kuti mupeze mwayi owina!

Kuti muwine ndi zophweka ngati 1-2-3;
1. Pangani Like page ya Altitude Technologies ya pa Facebook kapena ya pa Instagram
2. Pangani share post iyi pa wall panu ndi amzanu okwana 30 ayipange Like post mwapanga share yo, ndipo atsateso popanga Follow page yathu
3. Pangani post screenshot mu ma komenti pansipa ya meme yomwe mulinayo yomwe munasunga mu foni yomwe inakusangalasani kwambiri chaka chino

Screenshot yomwe izakhale ndi ma Like ambiri, kwa yemwe wakwanilisa 1 ndi 2 pamwambapo azawina mphoto ya imeneyi.

Mphotoyi ndi ya anthu okha okha wo ali a ku Malawi ndipo mpikisanuwu uzatha nthawi ya 12 koloko masana Lamulungu pa 31 December, 2023.

13/09/2023

Everything Launched at Appleโ€™s Wonderlust Event, in a 20 seconds clip.

03/02/2022

ThinkPad Yoga 370
256GB SSD Storage
8GB ram
Intel core i7 - 7th generation
14 inch 360ยฐ screen rotation
7ยฝ hrs battery ๐Ÿ”‹
Sim slot
Touchscreen
2.9ghz processor
Fingerprint scanner
With S pen ๐Ÿ–‹

K490,000

Want your business to be the top-listed Shop in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Address


Blantyre CBD
Blantyre

Opening Hours

Monday 08:00 - 17:00
Tuesday 08:00 - 17:00
Wednesday 08:00 - 17:00
Thursday 08:00 - 17:00
Friday 08:00 - 17:00
Saturday 09:00 - 17:00