Football Insight MW
Strictly Football
full time
ntaja socials 4-2 mangochi immigration socials
16/02/2026
bungwe la football association of Malawi tsopano latulusa mitengo ya Castel Challenge final ndipo ndi mmene ikuonekera mchithunzimo
02/02/2026
AMJIBA ATISIYA
Sapota wa FCB Nyasa Big Bullets, Rashid Chikumbutso Banda, kapena kuti amjiba, wamwalira atadwala kwa nthawi yochepa ndi nthenda yakuthamanga kwa magazi.
Banda, yemwe ankadziwika ndikuti 'Wanderers ikadzatenga league iye adzatalika' wamwalira m'mawa wa lero pa chipatala cha boma la Ntchisi.
Akubanja la malemuwa ndiomwe atsimikiza za imfayi.
A mjiba omwe anali ndi zaka 44 amachokera m'mudzi wa Chandawira, mfumu yaikulu Kalumo m'boma la Ntchisi.
02/02/2026
MWALE
FCB Nyasa Big Bullets have reached an agreement with Karonga United for the signing of goalkeeper Maclean MwaIe, subject to the opening of the transfer window.
The 27-year-old was instrumental for Karonga United during the 2025 TNM Super League season, registering 10 clean sheets in 28 appearances as the Northern Region side finished sixth on the table.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the business
Telephone
Website
Address
29, Kufa Road
Blantyre