ZWIDE

ZWIDE

Share

Real life talk | Money & daily struggles 🇲🇼
Best investment Relatable content every day Follow for more

07/07/2026

This option ndiyothekaso ndithu as a potential shareholder may choose not to take any action
Sikuti mumangodwa ai ndithu

06/07/2026

Kodi Tigule IPO?

Mwapita mu msika mwapeza 50kg yachimanga akupanga K45 000 anthu akugula komabe mosisitika

Inu muli nawo matumba anu 100 mufuna mugulits3 ndipo mufunaso mugulitse mukanthawinkochepa

Mungabwerese chimanga chanu chija nkuchigulitsa ma K50 000 per bag?
Same quality same quantity

Nditakhala ine nditha kubwera nkugulitsa pa K40 000 ngakhale pa K39 900 kuti ndipange attract ma ogula

Zotsatira zake mzoti ogula akabwera akangoona mitengo akangoona quality same same samgalimbaneso kuthamangira uko ndekuti adzadza kumene zagwa mtengoko

Awa ndi maganizo a ZWIDE

Want your business to be the top-listed Finance Company in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Telephone

Website

Address


Blantyre