Udabwa

Udabwa

Share

Udabwa

Advertising agency

Udabwa WhatsApp number 0996 76 67 60

16/07/2026

Wosayiwala kupephera kunja kuli asing'anga uku or amayiwala kuti sing'anga wamkulu ndi mulungu
Shalom 🙏

16/07/2026

Nthawi Zina zithu zikhoza kuvuta chifuka chofuna kufanana ndi ena ,,,,,,tisanafune kufanana ndi ena tiyen tiziyangane kuthekera kwathu ,,,,,osangot awa amalowa ma shop awa inenso mkalowemo mkagule ayi tiyen tipite misika yogwilizana ndi mmene titili ,,,,,Nthawi yokha imayakhula ndipo zimachitika mosakakamiza komanso mosafuna kufanana ndi wina.Shalom

16/07/2026

*Msika waung'ono kudera la Cape Maclear Ku Monkey Bay, wapsa chakumadzulo omwe ano.*

*Malingana ndi wapampando wa msikawu, a Godfrey Sozibele, chomwe chayambitsa motowu, sichikudziwika.*

*Iwo ati katundu ochuluka wapsa pa nthawi ya ngoziyi.*

16/07/2026

Chomwe chili changa chidzakhalabe changa, chomwe chili chanu chidzakhalabe chanu no matter how long it will take Koma Mulungu adzachikwanilitsa🙏🙏🙏🙏🙏

16/07/2026

osadikilanso kuti ena akumvetsetseni kapena kukukhulupilirani ayi zikhulupilireni nokha zimvetsetseni nokha mukadikila enawo muchedwa nazo nthawi yawo yoti akumvetsetseni ndi kukukhulupilirani sinakwane idzakwana mukachita bwino panopa nthawi yawo ndiyokusutsani pa chilichose munganene.

Photos from Udabwa's post 16/07/2026

Olo matamawo ndiyambira pati? Ndipo ulesiwo uchokera pati? Ndingafuneso kubwelera ku life iyiyi? Ine komwe ndikuchoka sindibisa kuti wina wake azilimbikitsika....sindidzasiya kulimbikitsa amphawi anzanga until nyengo zathu zisintheko tonse....

Nde olo muzindinyoza pano ndimangoseka🤣🤣🤣.apapa Malaya opatsidwa, nsapato zopatsidwa phee 🙈

Or anthu simumafuna kupangana support ine ndimava chisoni kwambri chifukwa palibe chimene chingatitheke patokha ine kundipangani support lero ndikuyenela tsiku Lina ndidzabweze pa zazikulu munandipangila zija

Wosakhala anthu asanje amphwawi azanga life ndi pang'onopang'ono

Inu muka comment ndikupanganso like zimandisangalatsa ndipo amene muli interesting ndi page ambuye azikudalitsani ine mtima othandiza ndili nawo koma ineso vuto ndiwochepekedwa

16/07/2026

kwanuko zimachitika kwandani izi 😁

16/07/2026

Zikafika apa mumatani?

16/07/2026

Ng'oooo
Chilibe mkazi icho😂

16/07/2026

Business advertising
Monitor+17+inch+ndipaseni+84k
Call+or+wap+0996 76 67 60
Lilongwe+kawale+2+

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Chilinde?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Address


Kawale 2
Chilinde