Prom Mw
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Prom Mw, Business service, Lilongwe.
21/07/2023
Wandani uyu
⛹️⛹️⛹️⛹️😆
You saw a T-shirt of K97, since you don't have cash you borrow K50 from your dad and K50 from your Mom.Now you have K100. You purchase aT-shirt for K97 and left with K3.00 change. You return K1 to your dad and K1 to your mom and keep the K1 for yourself. Now you owe your mom K49 and your dad K49. Added together
( K49+K49=K98) plus your K1=K99. Where is the missing K1???Please give me the answer. Ask around your friends. Ine mutu waima!!!
Chifukwa ndikuona ngati Alliance yaombapo K1
Like and follow my page 🙏🙏
*NKHATA-BAY*
*ZOOPSYA KU MZENGA MU BOMA LA NKHATABAY.*
Mpungwepungwe wabuka Ku mzenga Mdera la mfumu yaikulu Kabunduli pomwe bokosi la maliro lokhala ndi maina a wanthu lapezeka mmudzimo pafupi ndi Manda. Malinga ndi malipoti omwe atipeza, bokosilo ndi la saizi la khanda ndipo pamwamba pake Pali maina anai ndi mau oti anthuwo afe pa 12 June 2023. Mainawo ndi a 1. Alick Nkhata 2. Laban Mwase.3 Efraim Kabunduli 4.Grace Mwase. Ma lipoti akuti zimenezi achita ndi a Likita ndi mwana wawo Gracious kamba kofuna ufumu wa TA Kabunduli. Pakali Pano mpungwepungwe waukulu wabuka pankhani ya ufumu womwe umaynela kulongedwa lachisanu likubwerali koma akubanja atemetsa nkhwangwa pa mwala Kuti sangakhale ndi mfumu yopha anthu. Malinga ndi kafukufuku wathu, lero khamu la wanthu mosogozedwa ndi makolo a wanthu omwe maina awo Ali pa bokosilo akuyembekezeka kupita Ku police ndi Kwa DC Kuti akafunse nzeru poti zachitikazi nzoopsya.Anthu ambiri akwiya ndi nkhaniyi ndipo anenetsa Kuti a Likita ndi mwana wawo Gracious akuyenera afotokoze bwino.
📝NEWS UPDATE
Sugar parket 750 mu chipiku plus 😆
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the business
Website
Address
Lilongwe