Sims Learning Academy
Sims Learning Academy is a Platform designed teach Secondary and Tertiary Mathematics of all levels. [email protected]
(+265) 886655920 / 990998872
07/05/2026
Kodi muli ndimantha ndikusakonzekera koyenera kwamayeso anu a JCE komaso MSCE ๐ค๐ค ndipo muli ndikhumbokhumbo lofuna mutapeza thandizo lapaderadera muma Subject awa:
1. Additional Maths ๐งฎ
2. Ordinary Maths ๐งฎ
3. Chemistry ๐งช
4. Biology ๐งฌ
5. Physics โ๏ธ
6. Agriculture ๐ฝ and
7. Computer Studies? ๐ฉโ๐ป๐จโ๐ป ๐คท
Worry No More!!! Chifukwa ife a Sims Learning Academy tili ndi akaswili odziwa bwino Coaching komanso Teaching ๐๐๐ muma subject atelembawo kuti muchite bwino pamaeso anu ๐ง ๐ง ๐ง ๐
Anzanu tunena pano akuthadizika ndipo nkhawa zawo zamayeso zikunka natsika ๐ง ๐
Malo atsala ochepa ๐ค Lembetsani tsopano - Poti "Liwiro lamumchenga nkuyambira Limodz" ๐ฅ๐ฅ๐ฅ
FOR REGISTRATION: 0990998872/0990307299/0886655920
OR [email protected]
OR Join our WhatsApp Group using this Link ๐๏ธ๐
https://chat.whatsapp.com/I6OJiiC2WBSHKJxBS4pSGR?mode=gi_t
19/04/2026
Kodi mwana wanu (Inuyo) mukadakumana ndi vuto lopeza ma grade abwino? ๐ค๐ค๐ค Musadelenso nkhawa Chifukwa ife a Sims Learning Academy tikuthetsa mavuto amenewo!!! ๐ฅ๐ฅ๐ฅ
๐ Lowani ku ! komwe timaphunzitsa ma Subjects monga:
๐ Maths
๐งฌ Biology
๐งช Chemistry
โ๏ธ Physics
๐ต Agriculture
Makalasi onse (Form 1 - 4)
๐ฒ Phunzirani mosavuta pa foni kapena kompyuta yanu (mopanda stress, opanda kuyenda!)
๐ฅ Ife a Sims Learning Academy tili ndi aphunzitsi odziwa bwino ntchito ๐
Ndipo timapereka mayeso sabata iliyonse ๐ kuti tione kusintha kwanu ๐
๐ LEMBETSANI TSOPANO! poimba manambala ali mmusiwa:
๐ (+265) 886 655 920 / 990 307 299
โ ๏ธ Malo ndi ochepa!
๐ Lowani MWAMMANGUMMANGU asanadzaze!
Mwadzuka bwanji Kumeneko. maguy โจโจโจ
28/12/2025
Press Release ๐๐๐
18/12/2025
Shout out to our newest followers! Excited to have you onboard! G Man Thomas, Liaqat Ali Liaqat Ali, Onechojo Danjuma, Innock Felekisi
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Address
Likuni Avenue
Lilongwe
Opening Hours
| Monday | 07:00 - 17:00 |
| Tuesday | 07:00 - 17:00 |
| Wednesday | 07:00 - 17:00 |
| Thursday | 07:00 - 17:00 |
| Friday | 07:00 - 17:00 |
| Saturday | 07:30 - 12:00 |