InfoNow
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from InfoNow, Digital creator, Lilongwe.
24/04/2026
Mighty Wanderers FC yapeza jersey sponsorship partner watsopano ya ndalama yokwana 200 million kwa chaka kuchokera ku Kingbossi yomwe ndi yogulitsa njinga zamoto. Komano zikuoneka kuti ma "replica" jersey ambiri a consignment ya season ino omwe akugulitsidwa ali dominated ndi 888 bets yomwe zikumveka kuti ubale ndi noma unatha. Practically zikuthauza kuti team idzivala Kingbossi ma sapota 888 bets . Zaka ziwili zapitazo ma sapota amavala ma jersey osiyana ndi omwe ma player amavala yet pogulitsa ankati ndi ma "replica".
Ma "replica" a 888 anabwera ndi inprint yochoka ku factory and anali a season yomwe ino kusonyeza kuti sizinali zodzidzimukila. Kodi kwenikweni panavuta ndi pati kapena zimavuta pati?, Ndiye kuti 888 bets will get free advertising?, Komanso ndiye kuti aliyense obwera amafuna chizindikiro chake chidzikhala kutsogolo kwa jersey komanso large signage? Mosaphweketsa 200 mita, mwina ma team adzilola kit sponsorship ina idzipita ku training kit kapena pa arm.
Paja main sponsor wa league logo yake ikufunikanso pa front pompo 😊
21/04/2026
The Golden Era: When MDC United Owned the Pitch. Iyi ndiye imanyapula ma team. Squad ya achina Weston Chifutwe, Clement Kafwafwa, Chiyembekezo Zidana, Grant Lungu, Heston Munthali, Mapopa Msukwa, Thango Chauma, Chrispin Mpesi and others. Inali free scoring team. On this day in 2001 mu Chibuku Cup final MDC inamenya bullets 5-2 mu regulation time.
Tsiku ili Goalkeeper wa MDC Weston Chifutwe anapambadzidwa kunkhope ndi masapota a bullets akuchoka ku dressing room pa half time khani yokhudza "juju" kapena kuti research. Mbali inayi Swadick Sanudi aniyithawa game atachinyidwa zigoli ziwili za msanga mu mphindi zosaposa 12 kuchokera kwa Grant Lungu ndipo analowa Navigator Dzinkambani yemwe naye alandiranso zake zitatu. Pofika mphindi 6 ya mu second half MDC inali itachinya chigoli cha chisanu, eee kunavumba ma botolo sizinaoneke😃
Mighty Wanderers FC edged their arch-rivals FCB Nyasa Big Bullets 1–0 to lift the season-opening Charity Shield on Saturday at Bingu National Stadium in Lilongwe.
05/04/2026
Crop iyi atleast âš½
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the business
Telephone
Website
Address
Lilongwe