Awiri Beverages
We manufacture very tasty freezes in the following flavours:
1. Cola
2. Creme Soda
3. Raspberry
4. Orange
5. Pineapple
15/10/2025
Happy Mother's Day to all our customers ! Mwana mkazi thamanga basi, pakhomo pasasowe mchere.🔥🔥 Super Cool Freezes ndi dhilu 🔥
18/09/2024
Kunja ndiye kwatentha.....koma musade nkhawa!!Imwani Super Cool Freezes kuti mumve kayaziyazi!!
Dziko lonse linavomereza kale kuti freezes ndi m'modzi basi ndipo Super Cool!!
Super Cool! Ndiye freezes yo!!
05/09/2023
Kunja kwacha! Kunja kwatentha! Pezani phindu lochuluka, odani Super Cool Freezes lero. Pakhomo pasasowe sopo abale!
Tipezeni lero pakapenga ku Limbe kapena ku Lilongwe pafupi ndi pep store imene ili kuseli kwa Sana yapa Mzikiti.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the business
Telephone
Website
Address
Kamuzu Procession Road
Lilongwe
207201
Opening Hours
| 07:00 - 17:00 |