STRAS WORLD
World of fun and enjoyment
04/03/2026
TOASTT wa dropper diss to IKK kuseliku 🎵🔥
04/03/2026
Akuti iye sangamavale ma Skin jeans ngati anyamata a Chamba aku America..
Mayhoo anyozeka!!!
Mu interview Ina mkuluyi walankhula kuti akuti iyeyo ndi mamuna odziwa kutchena Asia Yonse.
Kim Jong Un, wanena kuti nthawi zambiri mkazi wake amamuyamikila kuti iyeyo amatchena kuponsa aliense ku Asia. "My wife says I am the most fashionable man in Asia"
"Izi zimandichititsa kukhala okondwa, ndimadziwa kuti anthu amakulemekeza ndi momwe ukuonekela. Ndiine m'tsogoleri wadziko lamphanvu, lotamika padziko lonse lapansi, osayembekezela kuti ndingavale tima skin jeans ngati anyamata aku Western, omwe amakamba zamisala mu nyimbo zawo. Ma trouser omwe ndimavala amayimila ulemu komanso ulamuliro." Adamaliza choncho m'tsogoleriyo...
LISTEN the Stras
Sunday lero tatiyeni timve mau achilimbikitso APA 🙏🙏🙏🙏
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the business
Telephone
Website
Address
Mzimba