Blada

Blada

Share

The Official page Of Blada.....Malawian Producer, Singer, Songwriter and Public Health Officer 🇲🇼 LifeStyle To Be On High

17/04/2026

SPECIAL ANNOUNCEMENT ❗

Oyimba ochokela boma la Ntcheu mukudziwitsidwa kuti mutenge nyimbo zanu mupite nazo ku AWUZE pa boma pa Ntcheu nthawi ya 3pm ,awa ndi oyimba ozungulila pa ntcheu paboma,koma omwe muli kutali ndi paboma imbani pa number iyi 0881620638.
Izi zikuchitika pamene Company ya MASSA ikufuna izithandiza oyimba koma ochokela ku Ntcheu.

Tiyeni Tikayese Mwayi

15/04/2026

UTHENGA ufike paliponse😀

Nyimbo ziyimbidwe mochuluka



#🗣️Blada!

Photos from Blada's post 09/04/2026

Are you willing to Buy a Car??

Ndi CHAPS MOTORS anthu akugula ma galimoto abwinotu pa mtengo wa bho, Just IMAGINE galimoto mukuyionayi ndi

Subaru Impreza 2014 model
Mileage 73000km
Lane assist
Automatic transmission
Good sound system

Machine amwene, akupita pa 25 Million yokha komaso NEGOTIABLE, Mukaona Certified Producer akuyendela MAZDA DEMIO musazati sindinanene 😄

For More Information Contact us :
+265 997 18 29 10 (Calls or Whatsapp)

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Ntcheu?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address


Mphate
Ntcheu