Zomba comunity tech college
s step to a brite future to young men an women with vocayion skills
31/10/2024
Chose your desired course today at Sakata Community Technical College.
Makwacha ochita kuwaona nokha awa musachedwe fulumilani kutila nkhobwe ndi mmawa.
Contact #0889831877 to get forms to apply
31/10/2024
2025 January intake
Nkhani ya bwino kwa achinyamatafe nonse ingakhalenso iwo pofuna kuwonjezela maphuzilo awo popeza nzelu za bussines, inutu monga mukudziwa paground pamafunika kuthamangathamanga ndi Sakata Community Technical College yakubweletselanitso maphuzilo a week end MA program monga Business administration management komanso accounting. Osaiwalanso form ya 2025 January intake form yatulukatu pangani machawi posankha course ya kuntima kwanu lelo kuti musazanong'oneze bondo pamawa
For more information visit on WhatsApp on 0889831877 to get forms
Do not hesitate anzanu akupeza malo
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Telephone
Website
Address
Zomba