Tabitha's Compassion International
Tabitha´s Compassion International
......responding to the cries from Honduras and Africa
12/20/2025
Bishop Pearson Nangwale a mpingo wa Grace Assembly International m'boma la Nsanje, ati ndi udindo wa mipingo kutenga gawo posamalira nkhosa zake mopitirira nkhani zauzimu.
Iwo ayankhula izi pomwe amakhazikitsa ntchito yoweta Mbuzi zomwe ati mabanja ovutika akhala akupatsirana zikayamba kuswana.
Malinga ndi a Nangwale, izi zithandizira ku ntchito yolimbikitsa kadyedwe koyenera komanso nkhani zachuma kwamabanja opindula omwe ndi a mu mpingo mwawo komanso madera amfumu Swale komwe akutumikira.
Kumbali yawo, a Omar Foote omwe amatsogolera bungwe la Tabitha Compassion lomwe lathandizira kuti ntchito yoweta Mbuziyi iyambike, ati ali ndichikhulupiriro kuti ntchitoyi isintha miyoyo ya anthu akuderali ndikuwamema kuti ayambe kutsatira Mulungu.
A Patrick Kopolo omwe ndi m'modzi mwa alangizi owona zachisamaliro cha anthu m'boma la Nsanje ati ntchitoyi ipititsa patsogolo chisamaliro cha anthu, maka osowa omwe mpingowu wati ndiomwe apindule ndi ndondomeko yopatsirana Mbuziyi.
Pakalipano, ulimiwu awuyamba ndi Mbuzi 15 zomwe azimangira khola lamakono ndipo ndalama zokwana K2 million ndizomwe zagwira ntchito.
Olemba:Precious Kadwala, Nsanje.
10/28/2025
🌍 Tabitha's Compassion International is dedicated to empowering communities in Honduras and Africa through education, poverty relief, and mission-driven projects.
Want to see the difference your support makes? Subscribe to our newsletter and follow our journey: https://mailchi.mp/tabithascompassion/newsletter
Learn more about our work: https://www.tabithascompassion.com/
hashtag hashtag hashtag hashtag hashtag
10/16/2025
We are heading to Africa again! We will be ministering in South Africa and Malawi. We need to raise $5000 in the next month. If you feel lead, please support our next trip in spreading the gospel to Africa. Click link to our giving
campaign----> https://givebutter.com/SDEtGY
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the organization
Telephone
Address
Catonsville, MD
21228