Oracle visual
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Oracle visual, Digital creator, Kamhlushwa, Nsanje.
26/03/2026
Ati "ndizamusintha ndekha" ungasinthe Hule waku Lunzu iwe?🤔
😂🤣😆💔💔🙌🙌
26/03/2026
Ku Chikwawa Bambo wina Amadwala kwambili ndipo Matenda ake Anali akachibweleza bweleza kuchila lero mawa adwala ndipo Banja lake limakhala la nkhawa koma iyeyu anati musadandaule ndikhala bwino.
Pakutha kwa masiku bambo aja anayitanitsa mwana wao womaliza ku badwa ndi Nkazi wake kumuuza kuti Ngati angamwalire Bokosi lake lidzatulukile Pa kona la nyumba lake ndipo mwana wake ndi mkazi wake anagwidwa ndi mantha koma anati nabola ndanena.
Ndipo zina chitikadi atamwalira mwambo unayenda moteromodi ngati mene ananenela mwini wake.
Mwakuganiza kwanu mukuganiza kuti adakasephanitsa Zomwe anawauza Chidakachitika ndi chani?
25/03/2026
Azimayi ambili Amalowa Bafa akuyimba nyimbo,Kusamba Akuyimba Nyimbo koma Pamazafike pena pake amazasiya kuyimba Kodi amakhala Akuchita chani.
Kenako nyimbo ija imadzapitiliranso🤣🤣🤣🤣🙌
25/03/2026
After kuthandizila kupha mzimayi nzake ndikumasekelera afterwards, amumbwandila.
_________
Mtsikana amene anatchuka ndi chithunzi choyambiliracho ali mu zebra 🦓 dress wagwidwa ndi a police dzulo pamodzi ndi anthu ena ochuluka omwe anathandizila kupha mzimayi wa business emwe anamunamizila kuti anaba katundu wina obisika wa pa thupi la m’nyamata wina, later atamufufuza m’nyamata uja zinapezeka kuti ndi zabodza koma mzimayi anali ataphedwa kale ndi gulu, a police agwila anthu opitilira 200 pa nkhaniyi (allegedly)
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Culinary Team
Attire
Telephone
Website
Address
Kamhlushwa
Nsanje