Agent Azeez

Agent Azeez

Share

Let's know more best of Malawi the real warm heart of Africa.

31/01/2026

Kwabadwa Mwana uku ndipo zadzetsa mpungwe pungwe Kwa makolo Maka maonekedwe amwanayu khungu ngat njoka .

26/01/2026

SAFUNA KUSIYA BIBI YAKE DZIKO LINA

Uyu ndi kim jong president waku North Korea

Iye amayenda ndi chimbuzi chake special cha golide akakhala ndi ulendo otuluka dziko kapena msonkhano mu dziko lake lomwe.

Chimbudzi ichi ndichosiyana ndi momwe mungayelekezere ndi cha president wathu waku Malawi Chifukwa kwathu kuno Chimbudzi cha president chimakhala galimoto special as a toilet yet cha Kim Jong ndichochita kunyamula nkumayenda nacho manja.

Izi zili choncho kamba ka chitetezo cha thupi lake kuti anthu ena asayeze DNA ya thupi lake

Sizokhazo Kim Jong akakhalira mpando ku meeting kapena msonkhano,ma bodyguard ayenera apupute malo omwe anakhalawo pogwilitsa ntchito ma chemicals ndicholinga choti pasakhale trace iliyonse ya president

Cup kapena glass la madzi lomwe president uyu wagwilitsa ntchito limayenera linyamulidwe nkupitisidwa kunyumba kwake apo ai aliphwanye kuti pasakhale trace iliyonse ya president uyu.

-Putin naye ake amanyamula mu Bag kapena mapepala

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Cape Town?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address


1 Victoria, Grassy Park
Cape Town
7888