Man Fu Comedy

Man Fu Comedy

Share

BEST COMEDIAN
come in numbers you will lough until your problem gone

21/05/2026

ALUKHU ANZANGA TIYENI KUMA COMMENT TIKATUKANE ATINYOZA

Mdulidwe wa ku chipatala ubwino wake nawu.

1. Umathandizira kupewa Ka chilombo Ka HIV

2. Kuteteza azimai ku Khansa ya khomo lachiberekero

3. Munthu odulidwa amakoma popanga s*x than osadulidwa

4. Munthu odulidwa amakhala ndi ukhondo ku chida chake

5 munthu odulidwa ali wachichepere amatha kukhala ndi chida chachikulu mwachilengedwe kusiyana ndi osadura

6 odula amatha kupanga control nyere pamene wosadura amangodzuka dzuka paliponse olo awone agalu akugonana umuona wadzuka chida chake

Tiyeni azibambo tikadulitse nthawi ikanalipo it's not too late kkkkk

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Cape Town?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address


Zomba , Eastern, Malawi
Cape Town
8001